Skip to content Skip to sidebar Skip to footer

(Download) "ULALIKI PA UTHENGA WABWINO WA MATEYU (III) - NDIWOTANI UTHENGA WABWINO OMWE UMAPANGITSA AKRISTU KUKHALA ANGWIRO?" by Paul C. Jong # eBook PDF Kindle ePub Free

ULALIKI PA UTHENGA WABWINO WA MATEYU (III) - NDIWOTANI UTHENGA WABWINO OMWE UMAPANGITSA AKRISTU KUKHALA ANGWIRO?

📘 Read Now     📥 Download


eBook details

  • Title: ULALIKI PA UTHENGA WABWINO WA MATEYU (III) - NDIWOTANI UTHENGA WABWINO OMWE UMAPANGITSA AKRISTU KUKHALA ANGWIRO?
  • Author : Paul C. Jong
  • Release Date : January 20, 2021
  • Genre: Christianity,Books,Religion & Spirituality,
  • Pages : * pages
  • Size : 1498 KB

Description

Mtumwi Mateyu amatiuza kuti Mawu a Yesu analankhulidwa ku wina aliyense mdzikoli lapansi, pakuti iye anaona Yesu ngati Mfumu ya mafumu. Tsopano, Akristu mdziko lonse, amene angobadwa mwatsopano mwa kukuhulupilira mu uthenga wa madzi ndi Mzimu umene timafalitsa, akufunitsitsadi kudya mkate wa moyo. Koma n’chobvuta kuti iwo akhale ndi chiyanjano limodzi ndi ife mu uthenga oona, cifukwa ali kutali kwambiri ndi ife. 

Chotero, kuti tikwanilitse zosowa za anthuwa za Yesu Khristu, Mfumu ya mafumu, ziphunzitso mu bukuli zakonzedwa ngati mkate wa moyo watsopano kuti iwo alimbitse kukula kwawo kwauzimu. Mlembi akunena kuti onse amene analindira chikhululukiro cha machimo awo mwa kukhulupilira mu Mawu a Yesu Khristu, Mfumu ya mafumu, afunika kudya Mawu Ake oyera kotero kuti ateteze chikhulupiliro chawo ndiponso kupitilizabe miyoyo yawo yauzimu. 

Bukuli lidzapereka mkate wauzimu weniweni wa moyo ku onse ainu amene anakhala anthu osatira Mfumu mwa chikhulupiliro. Kupitila mu M’pingo Wake ndiponso atumiki, Mulungu adzapitilizabe kumupatsani mkatewu wa umoyo. Lekani madalitso a Mulungu akhale pa inu nonse amene munabadwa mwatsopano mwa madzi ndi mwa Mzimu, amene ofunitsitsa kukhala ndi chiyanjano choona limodzi ndi ife mwa Khristu Yesu.


Free PDF Download "ULALIKI PA UTHENGA WABWINO WA MATEYU (III) - NDIWOTANI UTHENGA WABWINO OMWE UMAPANGITSA AKRISTU KUKHALA ANGWIRO?" Online ePub Kindle